User Registration

or Cancel
Breaking News

Latest News

01 October 2014

  Chief Justice Anastasia Msosa has cautioned magistrates and judges to be efficient when discharging their work following public concerns on the delayed and

01 October 2014

The Sherry party marks the commencement of the Michaelmas Session which is a new judiciary year. This year's event took place at the High Court

01 October 2014

  During her speech at this year's Sherry party on Wednesday October 1st, Chief Justice Anastasia Msosa assured that her office has made all

01 October 2014

  Parliament has passed four bills including authorizing government to borrow funds from OPEC fund for international development for the construction of cancer center

01 October 2014

  Carlsberg and Southern Bottlers Trade Union- CASOTU over the weekend held their Congress at Sun n’ Sand Holiday Resort in Mangochi.

Previous
Next
 • 01 October 2014
  Delayed judgments worry Chief Justice
 • 01 October 2014
  Sherry party 2014
 • 01 October 2014
  ‘Smooth progression on Cash-gate trials’
 • 01 October 2014
  Govt. to borrow funds from OPEC
 • 01 October 2014
  Mponda is CASOTU President

News in Brief

 1. Local News
 2. Business
 3. Politics
 4. Entertainment
 5. Sports
 6. International

Nkhani Zam'mabomma

29/09/14

29 September 2014

Mtsikana wina akataya bomwetamweta kamba ka mowaMtsikana wina ku Chigumula mu mzinda wa Blantyre wataya bomwetamweta mnyamata wina yemwe amafuna kumukwatira atamenyetsa nkhwangwa pa mwala kuti samukwatiranso atamupeza pa malo...

28/09/14

29 September 2014

Agona kudimba kamba kogwetsa mnyumbaMkulu wina ku Dambo la Nkhanga kwa Chipote mdela la mfumu Kachenga mboma la Balaka akuyenda mogwetsa nkhope yake pansi atamutulukila kuti akugona kudimba atagwetsa nyumba...

26/09/14

26 September 2014

Agwetsa maliro amumphasa popita kumandaMikoko yogona kwa Njobvu mboma la Kasungu yaima mitu akulu akulu achipembedzo china atagwetsa malilo omwe ananyamulila mu mphasa popita kumanda.

25/09/14

25 September 2014

Agwidwa akuchita chisembwere ndi mamuna wamwiniMayi wina ku Chingale mboma la Zomba amuphaphalitsa makofi atamupezelera akuchita zachisembwere ndi mwamuna wa mwini.

24/09/14

25 September 2014

Akakamira banja kamba ka mdulidweM’boma lomwelo la Thyolo koma m’dera la Mfumu Thomas , mwamuna wina wagwira njakata mkazi amene akufuna kumusiya ukwati atalumbira kuti sizitheka kuti banjalo lithe ati...

23/09/14

24 September 2014

Mayi wogulisa kaunjika ku Blantyre akunthidwa Mai wina ogulitsa nsapato za kaunjika ku Limbe mu mzinda wa Blantyre amuswa kodetsa nkhawa chifukwa chakhalidwe lake lokonda kuyenda ndi amuna a eni.

22/09/14

23 September 2014

Athawa kuchipinda osalipira ndalamaMwamuna wina waonekera ng’amba mtsikana wina woyenda yenda atamugwira pa msika wakwa Kachere mu mzinda wa Blantyre atathawa mchipinda china chogona anthu apa ulendo asanamulipire mayiyo.

21/09/14

22 September 2014

Alira koposa banja litatha Mayi wina kwa Senzani , mfumu yayikulu Phambala mboma la Ntcheu manja ali ku nkhondo chifukwa cha Chibwana chake chimene chapangitsa kuti banja lake lithe.

20/09/14

22 September 2014

Awutsa liwiro la mtondo odowoka kamba ka nyama ya njati Mkulu wina pafupi ndipa boma la Rumphi wadabwitsa anthu atapalasa njinga uku atamangilira dengu pa kaliyala kuthamangira ku Mjuma ku...

19/09/14

19 September 2014

Agwidwa Akuchita zachisembwere kudimba ndi mkazi wamwini Mkulu wina yemwe ali ndi golosale pa mudzi wa Saidi kwa mlumbe m’boma la Zomba amuswa kodetsa nkhawa atamugwila akuchita zachisembwele ndi mkazi...

TV

MBC Tv

MBC transmits a TV signal throughout Malawi via satellite and can be decoded through a 90cm antenna using any general
MBCtv

Radio

MBC Radio

MBC transmits a TV signal throughout Malawi via satellite and can be decoded through a 90cm antenna using any general

MBC Radio 1    |    MBC Radio 2

Advertise Here

Sports & Entertainment

Get Our Newsletter

Exchange Rates

Find us on Facebook