Azindikira kuti akudyetsedwa konda ine
Mwamuna wina wakwa Zinganguwo ku Sigelege mu mzinda wa Blantyre akuyenda ali khuma khuma, kudandaula atatulukira kuti mkazi wake adamudyetsa kondaine.
Chipwilikiti pa maliro
Kunali chipwilikiti pa maliro ena omwe anachitika m’mudzi wina kwa T/A Chadza mboma la Lilongwe pamene adzukulu anasemphana maganizo ndi Mfumu ya m’mudzimo.
Sing’anga agonana ndi mayi pochosa matsoka
Anthu a mdera lina mboma la Blantyre ati ndiokhumudwa kwambiri ndi zomwe anachita Sing’anga wina powumiliza kugonana ndi mayi wina ati pofuna kumuchotsa matsoka omwe akhala akukakamira mayiyo komanso ndikumuuza kuti agonanenso ndi mwamuna wake akuonerela.
Awona polekera kuchita zachimasomaso
Bambo wina wachimasomaso kwa T/A Chimombo mboma la Nsanje aona polekera atagonana ndi mtsikana yemwe bamboyo amayembekezera kuti aperekeze mdzukulu wake pokafunsila ukwati.