You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
02
July

02/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2241 times

Alandidwa phone ya m'manja kamba kochulusa zibwenzi
Mkulu wina kwa Kanduku mboma la Mwanza waona mbwadza mkazi wake atamulanda phone ya m’manja chifukwa chowirikiza zibwenzi.

02
July

01/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2300 times

Amuthamangitsa kubanja kamba kaumbombo
Bilidala wina ku Tsangano m’boma la Ntcheu akuyenda wela-wela ngati wataya singano mkazi wake atamuthamangitsa kuti sakumufuna banja kamba ka umbombo.

02
July

30/06/15 -

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2331 times

Njonda ina ithawa ili mbulanda
Njonda ina ya bizinezi ku Mloza m’boma la Mulanje inathawa ili mbulanda mnyumba ataipezelela ikuchita chisembwele ndi mkazi wa mwini.

29
June

29/06/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2386 times

Banja ndi ntchito zitha nthawi imodzi
Mkazi wina ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre akunong’oneza bondo banja lake komanso ntchito zitatha nthawi imodzi.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter