You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
29
May

26/06/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3317 times

Banja lisokonekela kamba ka kovinisa

Banja lina latekeseka m’dera la Mfumu Mkanda mboma la Mulanje mkulu wina atapeza mkazi wake akuvina ndi mphongo zina m’mudzimo.

29
May

25/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3099 times

Agwira nchiuno mwa munthu odwala

Anthu a m’mudzi mwa Likhonyowa  mboma la Machinga anatsala pang’ono kuthidzimula mkulu wina atamuzindikira kuti amagwira nchiuno mwa munthu odwala.

27
May

24/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3191 times

Athyole nthumba ndalama ya eni
Mkulu wina akuyenda mogwetsa nkhope yake pansi chifukwa cha manyazi mu mzinda wa Blantyre atamtulukila kuti anathyolela mthumba ndalama yomwe anamupatsa kuti akasiye ku banki.

27
May

23/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3473 times

Akuluakulu ena apita kumanda kufuna chakudya
Nyakwawa ina ku Chilomoni mu mzinda wa Blantyre yachenjeza adzukulu omwe akumakonda kupita kumanda akaona kuti chakudya chayandikila basi.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter