You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
14
May

14/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3867 times

Aletsedwa kulemba mayeso a std8
Anthu a m’mudzi wa Ng’ombezalira kwa Kaphuka mboma la Dedza ati ndiwokhumudwa komanso odabwa ndi zomwe achita akuluakulu owona za maphunzilo mderalo poletsa mtsikana wina wa std 8 kulemba nawo mayeso a chaka chino.

14
May

13/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 4058 times

Akolola chimanga cha eni
Mwamuna wina wapa mudzi wa Ndalama kwa Chitera m’boma la Chiradzulu yemwe wakwatira pa mudzi wa Malinga m’bomalo akuyenda wera-wera ngati wataya singano atamugwira akukolola chimanga m’munda mwa mbale wake.

12
May

12/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 4350 times

Kazizi tsakamuka kudenga pamapemphero
Mapemphero anasokonezeka mu mpingo wina kwa mfumu Kalonga m’boma la Salima , Kadzidzi wakufa atatsakamuka kudenga nkugwera m’busa yemwe amalalikira.

11
May

11/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3896 times

Amenya mayi ake kamba komanidwa nsima
Mnyamata wina wa Kumtumanje m’boma la Zomba wathawa atamenya mai ake mpaka kukomoka chifukwa choti mai akewo anamumana msima.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter