You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
30
July

30/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1914 times

Athamangitsidwa paukwati kamba kachiwerewere
Mai wina pamudzi wa Holowani kwa Kadewere mboma la Chiradzulu amuthamangitsa pa ukwati ku Lilongwe chifukwa chokonda chiwelewele mwamuna wake akatalikira pakhomo.

29
July

29/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1922 times

Athamangitsidwa pa ukwati kamba ka umbombo
Mkulu wina kwa Senzani mboma la Ntcheu amuthamangitsa pa ukwati chifukwa cha umbombo. Nkhaniyi ikuti mkuluyo anakwatira pamudzipo zaka ziwiri zapitazi koma mkaziyo anamupeza ndi ana akunjira awiri amuna okhaokha a zaka zosaposera khumi.

28
July

28/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2077 times

Mkazi wachibwenzi afika panyumba kuzasiya zovala
Mkulu wina wakwa Santhe pa msika mboma la Kasungu akuyenda moziya kwambili chifukwa cha manyazi, mkazi wa chibwenzi atadzamusiila zovala kuphatikizapo makabudula amkati pamaso pa mkazi wake.

27
July

27/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2063 times

Achilapa atakwera mumtengo ataledzera
Mkulu wina mdera la mfumu Nkalo mboma la Chiladzulu wanenetsa kuti sadzachitanso matama okwera mu mtengo ataledzera.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter