News In Brief
29
October

IT'S WORLD HABITAT, CITIES DAY

Written by
Published in News In Brief
Read 2050 times
Vice  President Dr  Saulos Chilima  presided over a joint commemoration of this year's World Habitat Day and World Cities Day in Lilongwe.
20
September

NCST SUPPORTS ICT ASSOCIATION

Written by
Published in News In Brief
Read 2760 times

The National Commission for Science and Technology (NCST) says it supports ICT Association of Malawi (ICTAM) in its efforts to offer ICT leadership. Director General of NCST Elijah Wanda said this in Lilongwe when the organization made a contribution of K2million to help ICTAM in its preparation for the 2021 ICT Expo. The EXPO is expected to provide a platform to local and international firms to showcase innovative and diversified products and services.

07
September

Mtsikana wina yemwe amagwila ntchito ya uphunzitsi pa sukulu ina ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota akulila usiku ndi usana mai ake omubala atamuthetsela banja.

Nkhani-yi ikuti mtsikana-yo atayamba ntchito anaganiza zokwatiwa koma amuna samamufunsila.  

Kenaka panamveka mphekesela yoti mai ake anamuchitila mankhwala kuti asakwatiwe ati poganiza kuti zonse zomwe amawachitila mai ake-wo asiya.  

Apa mtsikana-yo akuti naye anaganiza zopondaponda ndipo anapeza mtela omwe unakwanitsa kumumasula ku msinga za mai ake-wo.

Ndipo posakhalitsa mtsikana-yo anapeza banja.  Awiri-wa akuti anagwilizana kuti adzikhala mnyumba yomwe mtsikana-yo anamanga kwao.  

Koma mmalo mokondwa mai wa mtsikana-yo  kuti anayamba kupezela zifukwa mwamuna-yo ponena kuti ndi mphawi.  

Koma ngakhale mtsikana-yo anayesetsa kuikila kumbuyo mwamuna wake mkutemetsa nkhwangwa pa mwala kuti sasiyana ndi mwamuna-yo naye mai-yo anachita chotheka mpaka kuthetsa banja-lo.   


Mtsikana-yo akuti anadandaula kwambiri ndi zomwe mai ake anachita.   Koma patangotha miezi yochepa mtsikana-yo akuti anakwatiwanso ndi mkulu wina.   Mai wa mtsikana-yo mmalo mokondwa kuti mwamuna wa tsopano-yo yemwe anali wamakobili ake  akuti anapitiliza kuvutitsa mwana wake kuti athetse banja-lo.  


Mai-yo akuti anayamba kumalalatila mpongozi-yo pa maso ndipo mpongozi-yo atatopa ndi khalidwe-li anathetsa banja-lo.   Pakadali pano mtsikana-yo akuti akukhala khuma kamba ka zomwe mai ake amuchita. 

01
September

MP HAILS RAIPLY

Written by
Published in News In Brief
Read 3337 times

Parliamentarian for Nkhata Bay West Chrispin Chanju Mphande has hailed Raiply Limited for its commitment to introduce various developments in his area and Nkhatabay as a whole.

 

The parliamentarian was speaking during the launch of maintenance works on a 46-kilometer road from Lusangadzi to be done by Raiply Limited.

 

In his remarks, one of the officials from Raiply Limited Nathaniel Nthala said as a company, they believe in giving back to communities they are serving.

Page 1 of 41

Get Your Newsletter